Numeri 24:3, 4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako analankhula mwa ndakatulo kuti:+ “Mawu a Balamu mwana wa Beori,Mawu a mwamuna amene maso ake atseguka, 4 Mawu a munthu amene wamva mawu a Mulungu,Amene waona masomphenya a Wamphamvuyonse,Amene wagwada pansi, maso ake ali otsegula. Mawu ake akuti:+
3 Kenako analankhula mwa ndakatulo kuti:+ “Mawu a Balamu mwana wa Beori,Mawu a mwamuna amene maso ake atseguka, 4 Mawu a munthu amene wamva mawu a Mulungu,Amene waona masomphenya a Wamphamvuyonse,Amene wagwada pansi, maso ake ali otsegula. Mawu ake akuti:+