Salimo 110:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova adzatambasula ndodo yako yachifumu kuti ulamulirenso madera ena osati mu Ziyoni mokha. Iye adzanena kuti: “Pita pakati pa adani ako ndipo ukawagonjetse.”+ Aheberi 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma ponena za Mwana wake, iye akuti: “Mulungu ndi mpando wako wachifumu+ mpaka kalekale ndipo ndodo ya Ufumu wako, ndi ndodo yachilungamo.
2 Yehova adzatambasula ndodo yako yachifumu kuti ulamulirenso madera ena osati mu Ziyoni mokha. Iye adzanena kuti: “Pita pakati pa adani ako ndipo ukawagonjetse.”+
8 Koma ponena za Mwana wake, iye akuti: “Mulungu ndi mpando wako wachifumu+ mpaka kalekale ndipo ndodo ya Ufumu wako, ndi ndodo yachilungamo.