Numeri 22:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako Aisiraeli ananyamuka nʼkukamanga msasa mʼchipululu cha Mowabu, moyangʼanizana ndi Yeriko patsidya pa mtsinje wa Yorodano.+ Numeri 33:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Potsirizira pake ananyamuka kumapiri a Abarimu nʼkukamanga msasa ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, mʼchipululu cha Mowabu.+
22 Kenako Aisiraeli ananyamuka nʼkukamanga msasa mʼchipululu cha Mowabu, moyangʼanizana ndi Yeriko patsidya pa mtsinje wa Yorodano.+
48 Potsirizira pake ananyamuka kumapiri a Abarimu nʼkukamanga msasa ku Yeriko, pafupi ndi mtsinje wa Yorodano, mʼchipululu cha Mowabu.+