2 Samueli 22:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+ Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+ Salimo 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso amene amandipulumutsa.+ Mulungu wanga ndi thanthwe langa+ limene ndimathawirako,Iye ndi chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso* komanso malo anga othawirako otetezeka.*+ Salimo 19:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chilamulo cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa mphamvu.*+ Zikumbutso za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+ Yakobo 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwiro imachokera kumwamba.+ Imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zakuthambo,+ amene sasintha ngati mthunzi umene umasunthasuntha.+
31 Njira ya Mulungu woona ndi yangwiro.+Mawu a Yehova ndi oyengeka bwino.+ Iye ndi chishango kwa onse othawira kwa iye.+
2 Yehova ndi thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso amene amandipulumutsa.+ Mulungu wanga ndi thanthwe langa+ limene ndimathawirako,Iye ndi chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso* komanso malo anga othawirako otetezeka.*+
7 Chilamulo cha Yehova ndi changwiro,+ chimabwezeretsa mphamvu.*+ Zikumbutso za Yehova ndi zodalirika,+ zimapatsa nzeru munthu wosadziwa zinthu.+
17 Mphatso iliyonse yabwino ndi yangwiro imachokera kumwamba.+ Imatsika kuchokera kwa Atate wa zounikira zakuthambo,+ amene sasintha ngati mthunzi umene umasunthasuntha.+