Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 3:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Koma inu Yehova, mumanditeteza mbali zonse+ ngati chishango,

      Ndinu ulemerero wanga+ komanso ndinu amene mumatukula mutu wanga.+

  • Salimo 37:39, 40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+

      Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya mavuto.+

      40 Yehova adzawathandiza nʼkuwapulumutsa.+

      Adzawalanditsa kwa oipa nʼkuwapulumutsa,

      Chifukwa athawira kwa iye.+

  • Salimo 40:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Koma ine ndine munthu wovutika komanso wosauka.

      Yehova aone zimene zikundichitikira.

      Inu ndi amene mumandithandiza komanso kundipulumutsa.+

      Inu Mulungu wanga, musachedwe.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena