Salimo 78:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Kumene ankaweta nkhosa zoyamwitsa,Anamuika kuti akhale mʼbusa wa ana a Yakobo, omwe ndi anthu ake,+Ndi Isiraeli, amene ndi cholowa chake.+
71 Kumene ankaweta nkhosa zoyamwitsa,Anamuika kuti akhale mʼbusa wa ana a Yakobo, omwe ndi anthu ake,+Ndi Isiraeli, amene ndi cholowa chake.+