Hoseya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndani ali ndi nzeru? Amvetse zinthu zimenezi. Wochenjera ndani? Adziwe zimenezi. Njira za Yehova ndi zowongoka.+Ndipo anthu olungama adzayendamo,Koma olakwa adzapunthwa mʼnjira zimenezo.
9 Ndani ali ndi nzeru? Amvetse zinthu zimenezi. Wochenjera ndani? Adziwe zimenezi. Njira za Yehova ndi zowongoka.+Ndipo anthu olungama adzayendamo,Koma olakwa adzapunthwa mʼnjira zimenezo.