1 Samueli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Palibe woyera ngati Yehova,Palibenso wina koma inu nokha,+Ndipo palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+
2 Palibe woyera ngati Yehova,Palibenso wina koma inu nokha,+Ndipo palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+