Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 14:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Iye ankagulula mawilo a magaleta awo moti ankawayendetsa movutikira. Ndipo Aiguputo ankanena kuti: “Tiyeni tithawe pamaso pa Isiraeli, chifukwa Yehova akuwamenyera nkhondo yolimbana ndi Aiguputo.”+

  • 1 Samueli 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Apa ndiye zativuta ndithu. Ndi ndani atipulumutse mʼmanja mwa Mulungu wamkuluyu? Ameneyu ndi Mulungu amene anapha Aiguputo ambirimbiri mʼchipululu.+

  • Ezara 1:2, 3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Koresi mfumu ya Perisiya wanena kuti, ‘Yehova Mulungu wakumwamba wandipatsa maufumu onse apadziko lapansi.+ Iye wandituma kuti ndimumangire nyumba ku Yerusalemu+ mʼdziko la Yuda. 3 Aliyense amene ali pakati panu mwa anthu onse amene amamutumikira, Mulungu wake akhale naye ndipo apite ku Yerusalemu mʼdziko la Yuda nʼkukamanganso nyumba ya Yehova Mulungu wa Isiraeli. Iye ndi Mulungu woona ndipo nyumba yake inali ku Yerusalemu.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena