-
1 Akorinto 10:20, 21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ayi, koma ndikutanthauza kuti zinthu zimene anthu a mitundu ina amapereka nsembe amazipereka kwa ziwanda, osati kwa Mulungu.+ Ndipo sindikufuna kuti muzichita chilichonse chogwirizana ndi ziwanda.+ 21 Sizingatheke kuti muzimwa zamʼkapu ya Yehova* komanso zamʼkapu ya ziwanda. Sizingathekenso kuti muzidya “patebulo la Yehova”*+ komanso patebulo la ziwanda.
-