Numeri 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno Mose anayamba kufuulira Yehova kuti: “Chonde Mulungu wanga, muchiritseni chonde!”+ Yeremiya 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndichiritseni inu Yehova, ndipo ndidzachiradi. Ndipulumutseni ndipo ndidzapulumukadi,+Chifukwa ine ndimatamanda inu.
14 Ndichiritseni inu Yehova, ndipo ndidzachiradi. Ndipulumutseni ndipo ndidzapulumukadi,+Chifukwa ine ndimatamanda inu.