-
Chivumbulutso 10:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mngelo amene ndinamuona ataimirira panyanja ndi pamtunda uja, anakweza dzanja lake lamanja kumwamba. 6 Iye analumbira mʼdzina la Mulungu amene adzakhale ndi moyo mpaka kalekale,+ amene analenga kumwamba ndi zinthu zonse zimene zili kumeneko, dziko lapansi ndi zinthu zonse zimene zili mmenemo komanso nyanja ndi zinthu zonse zimene zili mmenemo.+ Analumbira kuti: “Nthawi yodikira yatha.
-