Numeri 20:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kumeneko, Mose anavula Aroni zovala zake zaunsembe nʼkuveka mwana wake Eleazara. Pambuyo pake, Aroni anamwalira pamwamba pa phiripo.+ Potsirizira pake, Mose ndi Eleazara anatsika mʼphirimo. Numeri 33:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Wansembe Aroni anakwera mʼphiri la Hora mogwirizana ndi zimene Yehova analamula, ndipo anamwalira mʼphirimo mʼchaka cha 40 mʼmwezi wa 5 pa tsiku loyamba la mweziwo kuchokera pamene Aisiraeli anatuluka mʼdziko la Iguputo.+
28 Kumeneko, Mose anavula Aroni zovala zake zaunsembe nʼkuveka mwana wake Eleazara. Pambuyo pake, Aroni anamwalira pamwamba pa phiripo.+ Potsirizira pake, Mose ndi Eleazara anatsika mʼphirimo.
38 Wansembe Aroni anakwera mʼphiri la Hora mogwirizana ndi zimene Yehova analamula, ndipo anamwalira mʼphirimo mʼchaka cha 40 mʼmwezi wa 5 pa tsiku loyamba la mweziwo kuchokera pamene Aisiraeli anatuluka mʼdziko la Iguputo.+