-
Numeri 20:12, 13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Pambuyo pake Yehova anauza Mose ndi Aroni kuti: “Chifukwa simunasonyeze chikhulupiriro mwa ine ndipo simunandilemekeze pamaso pa Aisiraeli, simudzalowetsa mpingowu mʼdziko limene ndidzawapatse.”+ 13 Madzi amenewo anatchedwa madzi a ku Meriba,*+ kumene Aisiraeli anakangana ndi Yehova ndipo anawasonyeza kuti iye ndi woyera.
-