Levitiko 22:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Musamadetse dzina langa loyera,+ mʼmalomwake muzindiona kuti ndine wopatulika pakati pa Aisiraeli.+ Ine ndine Yehova amene ndikukuyeretsani.+ Yesaya 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndi amene uyenera kumuona kuti ndi woyera,+Ndi amene uyenera kumuopa,Ndipo ndi amene uyenera kumulemekeza.”+
32 Musamadetse dzina langa loyera,+ mʼmalomwake muzindiona kuti ndine wopatulika pakati pa Aisiraeli.+ Ine ndine Yehova amene ndikukuyeretsani.+
13 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba ndi amene uyenera kumuona kuti ndi woyera,+Ndi amene uyenera kumuopa,Ndipo ndi amene uyenera kumulemekeza.”+