Ekisodo 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Mulungu analankhula mawu awa:+ Ekisodo 34:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Mose anakhalabe mʼphirimo ndi Yehova masiku 40, masana ndi usiku. Iye sanadye mkate kapena kumwa madzi.+ Ndipo Mulungu analemba mawu a pangano, Malamulo Khumi,* pamiyala yosemayo.+ Deuteronomo 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye anakuuzani pangano lake,+ kapena kuti Malamulo Khumi,*+ amene anakulamulani kuti muziwatsatira. Kenako analemba Malamulowo pamiyala iwiri yosema.+
28 Choncho Mose anakhalabe mʼphirimo ndi Yehova masiku 40, masana ndi usiku. Iye sanadye mkate kapena kumwa madzi.+ Ndipo Mulungu analemba mawu a pangano, Malamulo Khumi,* pamiyala yosemayo.+
13 Iye anakuuzani pangano lake,+ kapena kuti Malamulo Khumi,*+ amene anakulamulani kuti muziwatsatira. Kenako analemba Malamulowo pamiyala iwiri yosema.+