Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 18:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Zopereka zonse zopatulika zimene Aisiraeli azipereka kwa Yehova,+ ndakupatsa iwe ndi ana ako aamuna ndi aakazi, kuti likhale gawo lanu mpaka kalekale.+ Limeneli ndi pangano lamuyaya lamchere* limene Yehova akupanga ndi iwe komanso mbadwa zako.”

  • Deuteronomo 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Muzidzabweretsa zinthu zonse zimene ndikukulamulani kumalo amene Yehova Mulungu wanu adzasankhe kuti kukhale dzina lake.+ Muzidzabweretsa nsembe zanu zopsereza ndi nsembe zina, zopereka zanu za chakhumi,+ chopereka chochokera mʼmanja mwanu ndi nsembe zonse zimene mukupereka pokwaniritsa lonjezo limene munachita kwa Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena