-
Genesis 22:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Ndiyeno mngelo wa Yehova anaitana Abulahamu kachiwiri kuchokera kumwamba,
-
-
Genesis 26:3, 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ukhale ngati mlendo mʼdzikoli,+ ndipo ndidzapitiriza kukhala nawe ndi kukudalitsa, chifukwa mayiko onsewa ndidzawapereka kwa iwe ndi kwa mbadwa* zako.+ Ndidzakwaniritsa lumbiro limene ndinalumbira kwa bambo ako Abulahamu+ kuti: 4 ‘Ndidzachulukitsa mbadwa zako ngati nyenyezi zakumwamba,+ ndipo mayiko onsewa ndidzawapereka kwa mbadwa* zako.+ Mitundu yonse ya padziko lapansi idzapeza madalitso kudzera mwa mbadwa zako.’+
-