Genesis 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kanani anabereka Sidoni,+ mwana wake woyamba, kenako anabereka Heti.+ Genesis 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ahivi,+ Aariki, Asini, Genesis 34:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno Sekemu mwana wamwamuna wa Hamori Mhivi,+ mmodzi wa atsogoleri amumzindawu ataona mtsikanayu, anamutenga nʼkumugwiririra. Ekisodo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho ndipita kuti ndikawapulumutse mʼmanja mwa Aiguputo+ ndi kuwatulutsa mʼdzikolo nʼkuwalowetsa mʼdziko labwino komanso lalikulu, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Ndiwalowetsa mʼdziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+
2 Ndiyeno Sekemu mwana wamwamuna wa Hamori Mhivi,+ mmodzi wa atsogoleri amumzindawu ataona mtsikanayu, anamutenga nʼkumugwiririra.
8 Choncho ndipita kuti ndikawapulumutse mʼmanja mwa Aiguputo+ ndi kuwatulutsa mʼdzikolo nʼkuwalowetsa mʼdziko labwino komanso lalikulu, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Ndiwalowetsa mʼdziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+