Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Koma ndakusiya ndi moyo kuti ndikusonyeze mphamvu zanga komanso kuti dzina langa lilengezedwe padziko lonse lapansi.+

  • Ekisodo 15:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Munasonyeza chikondi chanu chokhulupirika potsogolera anthu amene munawawombola.+

      Ndi mphamvu zanu, mudzawatsogolera kudziko lanu lopatulika kumene mudzakhala.

      14 Anthu adzamva+ ndipo adzanjenjemera.

      Anthu okhala ku Filisitiya adzamva ululu.*

  • Yoswa 2:9, 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ndipo anawauza kuti: “Ndikudziwa kuti Yehova akupatsani dzikoli+ ndipo tonse tikuchita nanu mantha.+ Aliyense mʼdzikoli mtima wake suli mʼmalo chifukwa cha inu.+ 10 Tinamva mmene Yehova anaphwetsera madzi a Nyanja Yofiira pamene munkachoka ku Iguputo.+ Komanso mmene munaphera mafumu awiri a Aamori, Sihoni+ ndi Ogi,+ kutsidya* kwa mtsinje wa Yorodano.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena