Ekisodo 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwa kukoma mtima kwanu kosatha, mwatsogolera anthu amene munawawombola.+Mwa mphamvu yanu, inu mudzatengera anthu anu kudziko lanu lopatulika kumene mudzakhala.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:13 Yandikirani, tsa. 285
13 Mwa kukoma mtima kwanu kosatha, mwatsogolera anthu amene munawawombola.+Mwa mphamvu yanu, inu mudzatengera anthu anu kudziko lanu lopatulika kumene mudzakhala.+