Yoswa 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Tsopano Yoswa anali atakalamba ndiponso anali ndi zaka zambiri.+ Apa nʼkuti patapita masiku ambiri kuchokera pamene Yehova anapatsa Aisiraeli mpumulo+ powapulumutsa kwa adani awo onse owazungulira. Yoswa 24:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Patapita nthawi, Yoswa mwana wa Nuni, mtumiki wa Yehova, anamwalira ali ndi zaka 110.+
23 Tsopano Yoswa anali atakalamba ndiponso anali ndi zaka zambiri.+ Apa nʼkuti patapita masiku ambiri kuchokera pamene Yehova anapatsa Aisiraeli mpumulo+ powapulumutsa kwa adani awo onse owazungulira.