Ekisodo 19:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 ‘Inu munaona nokha zimene ndinachitira Aiguputo,+ kuti ndikunyamuleni pamapiko a chiwombankhanga nʼkukubweretsani kwa ine.+ Deuteronomo 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndi Yehova yekha amene anapitiriza kumutsogolera,*+Panalibe mulungu wachilendo amene anali naye.+
4 ‘Inu munaona nokha zimene ndinachitira Aiguputo,+ kuti ndikunyamuleni pamapiko a chiwombankhanga nʼkukubweretsani kwa ine.+