Machitidwe 7:15, 16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Yakobo anapita ku Iguputo+ kumene iye ndi makolo athu aja anafera.+ 16 Kenako mafupa awo anawatenga nʼkupita nawo ku Sekemu. Anakawaika mʼmanda amene Abulahamu anagula ndi ndalama zasiliva kwa ana a Hamori ku Sekemuko.+
15 Ndiyeno Yakobo anapita ku Iguputo+ kumene iye ndi makolo athu aja anafera.+ 16 Kenako mafupa awo anawatenga nʼkupita nawo ku Sekemu. Anakawaika mʼmanda amene Abulahamu anagula ndi ndalama zasiliva kwa ana a Hamori ku Sekemuko.+