Genesis 46:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yosefe anauza anthu kuti amukonzere galeta lake, kenako ananyamuka kuti akakumane ndi Isiraeli bambo ake ku Goseni. Atangofika kwa bambo akewo, nthawi yomweyo anawakumbatira nʼkulira kwa kanthawi.* Deuteronomo 26:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako muzikanena pamaso pa Yehova Mulungu wanu kuti, ‘Bambo anga anali munthu wongoyendayenda wa Chiaramu*+ ndipo anapita ku Iguputo+ ndi anthu ochepa amʼbanja lawo+ nʼkukakhala kumeneko monga mlendo. Koma ali kumeneko anakhala mtundu waukulu ndi wamphamvu.+
29 Yosefe anauza anthu kuti amukonzere galeta lake, kenako ananyamuka kuti akakumane ndi Isiraeli bambo ake ku Goseni. Atangofika kwa bambo akewo, nthawi yomweyo anawakumbatira nʼkulira kwa kanthawi.*
5 Kenako muzikanena pamaso pa Yehova Mulungu wanu kuti, ‘Bambo anga anali munthu wongoyendayenda wa Chiaramu*+ ndipo anapita ku Iguputo+ ndi anthu ochepa amʼbanja lawo+ nʼkukakhala kumeneko monga mlendo. Koma ali kumeneko anakhala mtundu waukulu ndi wamphamvu.+