Numeri 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Nadabu ndi Abihu anafa pamaso pa Yehova atapereka moto wosaloledwa kwa Yehova+ mʼchipululu cha Sinai, ndipo iwo anafa opanda ana. Pomwe Eleazara+ ndi Itamara+ anapitiriza kutumikira monga ansembe limodzi ndi Aroni bambo awo. Numeri 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mʼphirimo, ukamuvule Aroni zovala zake zaunsembe,+ nʼkuveka mwana wake Eleazara+ ndipo Aroni akamwalira kumeneko.”
4 Koma Nadabu ndi Abihu anafa pamaso pa Yehova atapereka moto wosaloledwa kwa Yehova+ mʼchipululu cha Sinai, ndipo iwo anafa opanda ana. Pomwe Eleazara+ ndi Itamara+ anapitiriza kutumikira monga ansembe limodzi ndi Aroni bambo awo.
26 Mʼphirimo, ukamuvule Aroni zovala zake zaunsembe,+ nʼkuveka mwana wake Eleazara+ ndipo Aroni akamwalira kumeneko.”