-
Oweruza 15:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Choncho Samisoni ananyamuka nʼkukagwira nkhandwe 300. Kenako anatenga nkhandwezo ziwiriziwiri nʼkuzimanga michira. Atatero, anaika muuni umodzi pakati pa michira iwiriyo. 5 Kenako anayatsa miyuniyo ndi moto, nʼkukusira nkhandwezo mʼminda ya Afilisti ya mbewu zosakolola. Choncho anayatsa chilichonse, kuyambira mitolo ya mbewu, mbewu zosakolola, minda ya mpesa komanso minda ya maolivi.
-