Yoswa 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Malire akumʼmawa a gawo la ana a Efuraimu motsatira mabanja awo anali awa: Kuchokera ku Ataroti-adara+ mpaka kukafika ku Beti-horoni Wakumtunda+
5 Malire akumʼmawa a gawo la ana a Efuraimu motsatira mabanja awo anali awa: Kuchokera ku Ataroti-adara+ mpaka kukafika ku Beti-horoni Wakumtunda+