Salimo 96:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamaso pa Yehova, chifukwa iye akubwera,*Iye akubwera kudzaweruza dziko lapansi. Adzaweruza anthu okhala padziko lapansi mwachilungamo+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+ Machitidwe 17:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ mwachilungamo dziko lonse lapansi, kudzera mwa munthu amene iye wamusankha. Ndipo watsimikizira anthu onse zimenezi pomuukitsa.”+
13 Pamaso pa Yehova, chifukwa iye akubwera,*Iye akubwera kudzaweruza dziko lapansi. Adzaweruza anthu okhala padziko lapansi mwachilungamo+Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mokhulupirika.+
31 Chifukwa wakhazikitsa tsiku limene akufuna kudzaweruza+ mwachilungamo dziko lonse lapansi, kudzera mwa munthu amene iye wamusankha. Ndipo watsimikizira anthu onse zimenezi pomuukitsa.”+