Luka 1:69 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 69 Iye watikwezera nyanga yachipulumutso*+ mʼnyumba ya mtumiki wake Davide,+ Machitidwe 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Zimenezi zinachitikadi pamene Herode, Pontiyo Pilato,+ anthu a mitundu ina komanso anthu a mu Isiraeli, anasonkhana mumzindawu nʼkuukira Yesu, mtumiki wanu woyera, amene inu munamudzoza.+
27 Zimenezi zinachitikadi pamene Herode, Pontiyo Pilato,+ anthu a mitundu ina komanso anthu a mu Isiraeli, anasonkhana mumzindawu nʼkuukira Yesu, mtumiki wanu woyera, amene inu munamudzoza.+