Salimo 132:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kumeneko ndidzachulukitsa mphamvu* za Davide. Wodzozedwa wanga ndamukonzera nyale.+