Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iye analonjeza kuti: “Inu Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, mukaona kuvutika kwa ine kapolo wanu nʼkundikumbukira ndiponso mukapanda kundiiwala ine kapolo wanu nʼkundipatsa mwana wamwamuna,+ ndidzamʼpereka kwa Yehova masiku onse a moyo wake ndipo lezala silidzadutsa mʼmutu mwake.”+

  • 1 Samueli 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pa nthawi imeneyo, mwana uja Samueli ankatumikira+ Yehova moyangʼaniridwa ndi Eli. Koma mawu a Yehova anali osowa masiku amenewo ndipo anthu sankaona masomphenya+ pafupipafupi.

  • 1 Samueli 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Samueli anagonabe mpaka mʼmawa. Atadzuka anatsegula zitseko za nyumba ya Yehova, koma ankaopa kuuza Eli za masomphenya amene anaona.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena