Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 15:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Chifukwa chakuti wanyoza mawu a Yehova komanso waphwanya lamulo lake, munthuyo aziphedwa ndithu.+ Aziyankha mlandu wa tchimo lakelo.’”+

  • 1 Samueli 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Atumikiwa ankachimwira Yehova kwambiri,+ chifukwa sankalemekeza nsembe ya Yehova.

  • 1 Samueli 3:13, 14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Umuuze kuti ndidzaweruza nyumba yake mpaka kalekale chifukwa cha zinthu zolakwika zimene iye akuzidziwa.+ Ana ake akunyoza Mulungu+ koma sakuwadzudzula.+ 14 Nʼchifukwa chake ndalumbirira nyumba ya Eli kuti machimo a anthu a mʼnyumba ya Eli sadzaphimbidwa ndi nsembe ina iliyonse.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena