Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 28:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 “Pakati pa Aisiraeli, usankhe Aroni+ mʼbale wako pamodzi ndi ana ake+ Nadabu, Abihu,+ Eleazara komanso Itamara+ kuti atumikire monga ansembe anga.

  • Levitiko 8:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pomaliza Mose anathira ena mwa mafuta odzozera pamutu pa Aroni nʼkumudzoza kuti akhale wopatulika.+

  • Numeri 17:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndodo ya munthu amene ndimusankheyo+ idzaphuka, ndipo ndidzathetsa kungʼungʼudza kwa Aisiraeli kumene akuchita motsutsana ndi ine+ komanso motsutsana ndi iwe.”+

  • Numeri 17:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tsiku lotsatira, Mose atalowa mʼchihema cha Umbonicho, anangoona kuti ndodo ya Aroni yoimira nyumba ya Levi yaphuka. Ndodoyo inali itaphuka ndipo inkamasula maluwa komanso kubereka zipatso za amondi zakupsa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena