1 Samueli 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komanso Likasa la Mulungu linalandidwa, ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana a Eli, anaphedwa.+ 1 Samueli 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu amene anabwera ndi uthengayo anati: “Aisiraeli athawa Afilisiti, ndipo agonjetsedwa koopsa.+ Ana anunso awiri, Hofeni ndi Pinihasi, aphedwa.+ Komanso Likasa la Mulungu woona lalandidwa.”+
17 Munthu amene anabwera ndi uthengayo anati: “Aisiraeli athawa Afilisiti, ndipo agonjetsedwa koopsa.+ Ana anunso awiri, Hofeni ndi Pinihasi, aphedwa.+ Komanso Likasa la Mulungu woona lalandidwa.”+