Ekisodo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mundipangire malo opatulika, ndipo ndidzakhala pakati panu.+ 1 Samueli 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nyale ya Mulungu+ inali isanazimitsidwe, ndipo Samueli anali atagona mʼkachisi*+ wa Yehova mmene munali Likasa la Mulungu. 2 Samueli 7:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiyeno mfumuyo inauza mneneri Natani+ kuti: “Ine ndikukhala mʼnyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene Likasa la Mulungu woona likukhala mutenti.”+
3 Nyale ya Mulungu+ inali isanazimitsidwe, ndipo Samueli anali atagona mʼkachisi*+ wa Yehova mmene munali Likasa la Mulungu.
2 Ndiyeno mfumuyo inauza mneneri Natani+ kuti: “Ine ndikukhala mʼnyumba ya mitengo ya mkungudza,+ pamene Likasa la Mulungu woona likukhala mutenti.”+