Salimo 55:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Umutulire Yehova nkhawa zako,+Ndipo iye adzakuthandiza.+ Iye sadzalola kuti munthu wolungama agwe.*+ Salimo 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+
22 Umutulire Yehova nkhawa zako,+Ndipo iye adzakuthandiza.+ Iye sadzalola kuti munthu wolungama agwe.*+