Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 37:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Lola kuti Yehova akutsogolere panjira yako,*+

      Uzimudalira ndipo iye adzakuthandiza.+

  • Salimo 68:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Atamandike Yehova, amene amanyamula katundu wathu tsiku ndi tsiku,+

      Mulungu woona amene amatipulumutsa. (Selah)

  • Afilipi 4:6, 7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Musamade nkhawa ndi chinthu chilichonse.+ Mʼmalomwake, nthawi zonse muzipemphera kwa Mulungu, muzimuchonderera kuti azikutsogolerani pa chilichonse ndipo nthawi zonse muzimuthokoza.+ 7 Mukatero, mtendere+ wa Mulungu umene anthu sangathe kuumvetsa, udzateteza mitima yanu+ ndi maganizo anu pamene mukutsatira Khristu Yesu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena