1 Mafumu 3:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Aisiraeli onse anamva mmene mfumu inaweruzira nkhaniyo ndipo anachita mantha ndi mfumuyo+ chifukwa anaona kuti Mulungu wamupatsa nzeru kuti aziweruza mwachilungamo.+ Mlaliki 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuwonjezera pa kukhala ndi nzeru, wosonkhanitsa anthuyu nthawi zonse ankaphunzitsa anthuwo zimene iye ankadziwa+ ndipo anaganizira mozama komanso anafufuza zinthu mosamala kuti alembe* miyambi yambiri.+
28 Aisiraeli onse anamva mmene mfumu inaweruzira nkhaniyo ndipo anachita mantha ndi mfumuyo+ chifukwa anaona kuti Mulungu wamupatsa nzeru kuti aziweruza mwachilungamo.+
9 Kuwonjezera pa kukhala ndi nzeru, wosonkhanitsa anthuyu nthawi zonse ankaphunzitsa anthuwo zimene iye ankadziwa+ ndipo anaganizira mozama komanso anafufuza zinthu mosamala kuti alembe* miyambi yambiri.+