Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 10:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ana a Yavani anali Elisha,+ Tarisi,+ Kitimu+ ndi Dodanimu.

  • Salimo 72:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mafumu a ku Tarisi komanso amʼzilumba adzapereka msonkho.+

      Mafumu a ku Sheba ndi ku Seba adzapereka mphatso.+

  • Ezekieli 27:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tarisi+ ankachita nawe malonda chifukwa unali ndi chuma chochuluka.+ Anakupatsa siliva, chitsulo, tini ndi mtovu kuti atenge katundu wako.+

  • Yona 1:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Koma Yona ananyamuka nʼkulowera ku Tarisi, kuthawa Yehova. Atafika ku Yopa anapeza chombo chopita ku Tarisi. Iye analipira ndalama za ulendowo pothawa Yehova nʼkukwera chombocho kuti apite ku Tarisi limodzi ndi anthu amene anali mmenemo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena