1 Mafumu 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mfumuyo inapanganso mpando wachifumu waukulu waminyanga ya njovu+ nʼkuukuta ndi golide woyenga bwino.+
18 Mfumuyo inapanganso mpando wachifumu waukulu waminyanga ya njovu+ nʼkuukuta ndi golide woyenga bwino.+