Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Koma mukapanda kumvera mawu a Yehova Mulungu wanu poonetsetsa kuti mukutsatira malamulo ake onse ndi malangizo ake amene ndikukupatsani lero, mudzatembereredwa ndipo zinthu zoipa zotsatirazi zidzakuchitikirani:+

  • Deuteronomo 28:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Thambo limene lili pamwamba pa mutu wanu lidzakhala ngati kopa,* ndipo nthaka yanu idzakhala ngati chitsulo.+

  • Yeremiya 14:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Kodi pa mafano opanda pake a mitundu ya anthu pali fano lililonse limene lingagwetse mvula?

      Kapena kodi kumwamba pakokha kungagwetse mvula yamvumbi?

      Kodi si inu nokha, Yehova Mulungu wathu, amene mumachititsa zimenezi?+

      Chiyembekezo chathu chili mwa inu

      Chifukwa inu nokha ndi amene mumachita zonsezi.

  • Luka 4:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Mwachitsanzo, ndithu ndikukuuzani kuti: Munali akazi ambiri amasiye mu Isiraeli mʼmasiku a Eliya, pamene kumwamba kunatsekedwa kwa zaka zitatu ndi miyezi 6 ndipo mʼdziko lonse munali njala yaikulu.+

  • Yakobo 5:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Eliya anali munthu ngati ife tomwe, komabe atapemphera kuchokera pansi pamtima kuti mvula isagwe, mvula sinagwedi mʼdzikolo kwa zaka zitatu ndi miyezi 6.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena