1 Mafumu 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Patapita nthawi, mʼchaka chachitatu,+ Eliya anamva mawu a Yehova akuti: “Pita ukaonekere kwa Ahabu, chifukwa ndikufuna kubweretsa mvula mʼdzikoli.”+
18 Patapita nthawi, mʼchaka chachitatu,+ Eliya anamva mawu a Yehova akuti: “Pita ukaonekere kwa Ahabu, chifukwa ndikufuna kubweretsa mvula mʼdzikoli.”+