Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 22:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kenako iwo anafika pamalo amene Mulungu woona anamuuza Abulahamu. Atafika pamalowo, iye anamanga guwa lansembe nʼkuyala nkhuni zija paguwapo. Atatero, anamanga Isaki mwana wakeyo manja ndi miyendo nʼkumugoneka paguwapo, pamwamba pa nkhuni.+

  • Levitiko 1:7, 8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Ana a Aroni, ansembe, aziika moto paguwa lansembelo+ nʼkuyalapo nkhuni. 8 Ndiyeno ana a Aroni ansembe, aziyala nyama yoduladulayo+ pankhuni zimene zili pamoto wapaguwa lansembepo. Aziyala nyamayo pamodzi ndi mutu ndiponso mafuta.*

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena