-
Ekisodo 34:5, 6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Yehova anatsika+ mumtambo nʼkuima pafupi ndi Mose ndipo analengeza dzina lake lakuti Yehova.+ 6 Ndiyeno Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wokoma mtima,*+ wosakwiya msanga+ ndiponso wachikondi chokhulupirika chochuluka+ komanso choonadi.*+
-