Hoseya 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tsopano iwo akuchita machimo ena,Ndipo akugwiritsa ntchito siliva wawo popanga zifaniziro zachitsulo.+Amapanga mafano mwaluso, koma zonsezi ndi ntchito za amisiri. Iwo amauza mafanowo kuti, ‘Amuna opereka nsembe akise mafano a ana angʼombe.’+
2 Tsopano iwo akuchita machimo ena,Ndipo akugwiritsa ntchito siliva wawo popanga zifaniziro zachitsulo.+Amapanga mafano mwaluso, koma zonsezi ndi ntchito za amisiri. Iwo amauza mafanowo kuti, ‘Amuna opereka nsembe akise mafano a ana angʼombe.’+