-
1 Akorinto 9:14, 15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Komanso Ambuye analamula kuti anthu amene amalalikira uthenga wabwino azipeza zofunika pa moyo kudzera mu uthenga wabwino.+
15 Koma sindinagwiritsepo ntchito ufulu umenewu.+ Ndiponso sikuti ndalemba zimenezi kuti ndiyambe kugwiritsa ntchito ufuluwu, chifukwa zingakhale bwino kuti ineyo ndife, kusiyana nʼkuti . . . palibe munthu amene angandilande zifukwa zomwe ndikudzitamira!+
-