7 Choncho muzikhala mʼnyumba imeneyo+ ndipo muzidya ndi kumwa zimene angakupatseni,+ chifukwa wantchito ayenera kulandira malipiro ake.+ Musamachoke kumene mwafikirako nʼkupita kunyumba zina.
8 Komanso mukalowa mumzinda ndipo iwo nʼkukulandirani, muzidya zimene akukonzerani,