Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 2:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ndiyeno Sanibalati wa ku Beti-horoni, Tobia+ mtumiki wa Chiamoni+ ndi Gesemu Mluya+ atamva zimenezi anayamba kutiseka ndi kutinyoza.+ Iwo anati: “Nʼchiyani chimene mukuchitachi? Kodi mukugalukira mfumu?”+

  • Nehemiya 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tobia+ Muamoni,+ yemwe anaima pambali pake anati: “Ngakhaletu nkhandwe itakwera pampanda wamiyala umene akumangawo ikhoza kuugwetsa.”

  • Nehemiya 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Inu Mulungu wanga, kumbukirani Tobia+ ndi Sanibalati komanso zimene anachitazi. Mukumbukirenso Nowadiya mneneri wamkazi ndi aneneri onse amene ankafuna kundiopseza.

  • Nehemiya 13:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako ndinafika ku Yerusalemu ndipo ndinaona zoipa zimene Eliyasibu+ anachita popatsa Tobia+ chipinda mʼbwalo la nyumba ya Mulungu woona.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena