Levitiko 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ana a Aroni, ansembe, aziika moto paguwa lansembelo+ nʼkuyalapo nkhuni. Levitiko 6:12, 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Moto wapaguwa lansembe uziyaka nthawi zonse. Usamazime. Wansembe aziikapo nkhuni+ mʼmawa uliwonse nʼkuikapo nsembe yopsereza. Akatero aziwotcha mafuta a nsembe yamgwirizano pamotopo.+ 13 Motowo uziyaka nthawi zonse paguwa lansembe. Usamazime.
12 Moto wapaguwa lansembe uziyaka nthawi zonse. Usamazime. Wansembe aziikapo nkhuni+ mʼmawa uliwonse nʼkuikapo nsembe yopsereza. Akatero aziwotcha mafuta a nsembe yamgwirizano pamotopo.+ 13 Motowo uziyaka nthawi zonse paguwa lansembe. Usamazime.